×
Image

MALAMULO OFUNIKIRA KWA MSILAMU - (Chichewa)

MALAMULO OFUNIKIRA KWA MSILAMU

Image

Mtumiki wa Chisilamu Muhammad - Allah amuchitire chisoni ndi kumpatsa mtendere - (Chichewa)

Mtumiki wa Chisilamu Muhammad - Allah amuchitire chisoni ndi kumpatsa mtendere

Image

Kukamba zokhuza chikhulupiliro cha chisilamu mwa chidule - (Chichewa)

Kukamba zokhuza chikhulupiliro cha chisilamu mwa chidule

Image

Zomwe Msilamu sakuyenera kuti asazidziwe - (Chichewa)

Zomwe Msilamu sakuyenera kuti asazidziwe

Image

Njira zothandizira kukhala moyo wachimwemwe - (Chichewa)

No Description

Image

TANTHAWUZO LACHISILAMU M’CHICHEWA - (Chichewa)

-

Image

chikulupi cha uislamu - (Chichewa)

Ndithu matamando onse ndi a Allah, tikumutamanda, kumpempha chithandizo ndi kumpempha chikhululuko, komanso tikuzichinjiriza mwa Allah ku zoyipa za mitima ndi ntchito zathu. Amene Allah wamuongola palibe angamusocheretse, ndipo amene wasochera palibe angamuongole. Ndikuchitira umboni kuti palibe mulungu wina (woyenera kupembedzedwa) koma Allah, Wayekha, wopanda wothandizana naye. Ndikuchitiranso umboni kuti....

Image

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa - (Chichewa)

Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu, aumve m’chilankhulo chawo cha Chichewa. Choncho ntchitoyi idagwirikadi kotero kuti munthu akawerenga bwinobwino akhoza kumva uthenga wa Mulungu m’Qur’an. Ndayetsetsa m’kutanthauzira kwanga....

Image

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi - (Chichewa)

QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi

Image

Buku la Ndondomeko ya Swalat (Tarteeb Swalaat) - (Chichewa)

Mu buku ili muli makomo awa: Kufunika kwa Swalaat, lamulo lake komanso zoyenereza kuti swalaat itheke. Machitidwe a wudhu kudzera m’zithunzi zolongosola bwino, kenako Sunnah za wudhu komanso zomwe zimaononga wudhu. Mu bukuli mulinso mapangidwe a Adhaan ndi Iqaamah, mapangidwe a swalaat kudzera m’zithunzi zolongosola bwino, komanso muli khomo la....

Image

MAPATA ATATU - (Chichewa)

-

Image

CHIKHULUPILIRO CHA MSILAMU - (Chichewa)

Buku ili likukamba nsanamira zisanu ndi chimodzi za chikhulupiliro cha Msilamu. Layamba ndi kukamba mwachidule zomwe Msilamu amakhulupilira nthawi zonse, kenako lakamba zakomwe chikhulupilirochi chikuchokera (Qur’an ndi Sunnah). Nsanamira zimenezi ndimonga: Kukhulupilira Allah Yekha, kukhulupilira Angelo, kukhulupilira Mabuku a Allah, kukhulupilira Atumiki a Allah, kukhulupilira Tsiku Lachiweruzi ndinso kukhulupilira Chikhonzero....