MALAMULO OFUNIKIRA KWA MSILAMU
MALAMULO OFUNIKIRA KWA MSILAMU - (Chichewa)
chikulupi cha uislamu - (Chichewa)
Ndithu matamando onse ndi a Allah, tikumutamanda, kumpempha chithandizo ndi kumpempha chikhululuko, komanso tikuzichinjiriza mwa Allah ku zoyipa za mitima ndi ntchito zathu. Amene Allah wamuongola palibe angamusocheretse, ndipo amene wasochera palibe angamuongole. Ndikuchitira umboni kuti palibe mulungu wina (woyenera kupembedzedwa) koma Allah, Wayekha, wopanda wothandizana naye. Ndikuchitiranso umboni kuti....
QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’chichewa - (Chichewa)
Chifukwa chakufunika kwa uthengawu kuti ufike kwa anthu onse, a Bungwe la Africa Muslim Agency adandipempha kuti ndimasulire Qur’an m’chichewa, ndicholinga chakuti amene sangathe kumvetsa uthenga wake m’chiarabu, aumve m’chilankhulo chawo cha Chichewa. Choncho ntchitoyi idagwirikadi kotero kuti munthu akawerenga bwinobwino akhoza kumva uthenga wa Mulungu m’Qur’an. Ndayetsetsa m’kutanthauzira kwanga....
QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi - (Chichewa)
QUR’AN YOLEMEKEZEKA yotanthauzidwa m’Chichewa ndi
Buku la Ndondomeko ya Swalat (Tarteeb Swalaat) - (Chichewa)
Mu buku ili muli makomo awa: Kufunika kwa Swalaat, lamulo lake komanso zoyenereza kuti swalaat itheke. Machitidwe a wudhu kudzera m’zithunzi zolongosola bwino, kenako Sunnah za wudhu komanso zomwe zimaononga wudhu. Mu bukuli mulinso mapangidwe a Adhaan ndi Iqaamah, mapangidwe a swalaat kudzera m’zithunzi zolongosola bwino, komanso muli khomo la....
MAPATA ATATU - (Chichewa)
-
CHIKHULUPILIRO CHA MSILAMU - (Chichewa)
Buku ili likukamba nsanamira zisanu ndi chimodzi za chikhulupiliro cha Msilamu. Layamba ndi kukamba mwachidule zomwe Msilamu amakhulupilira nthawi zonse, kenako lakamba zakomwe chikhulupilirochi chikuchokera (Qur’an ndi Sunnah). Nsanamira zimenezi ndimonga: Kukhulupilira Allah Yekha, kukhulupilira Angelo, kukhulupilira Mabuku a Allah, kukhulupilira Atumiki a Allah, kukhulupilira Tsiku Lachiweruzi ndinso kukhulupilira Chikhonzero....
CHIDULE CHOFOTOKOZA ZA KACHITIDWE ΚΑ MAPEMPHERO A UMRAH
Buku ili lasonkhanitsa kakhalidwe kwa amayi m’zipembedzo zitatu: Chiyuda, Chikristu ndi Chisilamu. Bukuli lalongosola mfundo zofunikira zochokera mu Chiyuda, komwe mzimayi sanangomutchula kuti ndi wochimwa, koma anatinso ndiyemwe anamuchimwitsa mwamuna. Koma Qur’an ili ndi kuwona kosiyana ndi mabuku ena onse, poti imamuona mzimai kuti ndi wofunikira kwambiri pa chitukuko cha....
KULONGOSOLA MAHADITH 40 A MNENERI (SAW) KWA ACHINYAMATA

API
